1 Mafumu 7:32 BL92

32 Ndipo njinga zinai zinali pansi pa matsekerezo, ndi mitanda ya njinga inali m'mphakamo, ndi msinkhu wa njinga imodzi unali mkono umodzi ndi nusu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 7

Onani 1 Mafumu 7:32 nkhani