1 Mafumu 7:39 BL92

39 Ndipo anaika maphaka asanu ku dzanja lamanja la nyumba, ndi maphaka asanu ku dzanja lamanzere la nyumba; naika thawalelo ku dzanja lamanja la nyumba kum'mawa kupenya kumwera.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 7

Onani 1 Mafumu 7:39 nkhani