47 Ndipo Solomo anazileka zipangizo zonse osaziyesa, popeza zinacuruka ndithu; kulemera kwace kwa mkuwa wonsewo sikunayeseka.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 7
Onani 1 Mafumu 7:47 nkhani