1 Mafumu 7:50 BL92

50 ndi zikho, ndi zozimira nyali, ndi mbale, ndi zipande, ndi zopalira mota za golidi woyengetsa, ndi zomangira zitseko zagolidi, za zitseko za cipinda ca m'katimo, malo opatulikitsa, ndiponso za zitseko za nyumba ya Kacisi.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 7

Onani 1 Mafumu 7:50 nkhani