1 Mafumu 7:8 BL92

8 Ndipo nyumba yace yakukhalamo iye, m'bwalo lina la m'tsogolo mwa khumbilo, linamangidwa cimodzimodzi. Anammangiranso nyumba mwana wamkazi wa Farao, amene adamkwatira Solomo, yofanafana ndi khumbi limeneli.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 7

Onani 1 Mafumu 7:8 nkhani