1 Mafumu 8:19 BL92

19 Koma usamange ndiwe nyumbayo, koma mwana wako adzaturuka m'cuuno mwako, iyeyo adzamangira dzina langa nyumba.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8

Onani 1 Mafumu 8:19 nkhani