1 Mafumu 8:50 BL92

50 ndi kukhululukira anthu anu adacimwira Inu ndi mphulupulu zao zonse adaparamula nazo kwa Inu; ndipo muwacititsire cifundo iwo amene anawagwira ndende, kuti awacitire cifundo;

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8

Onani 1 Mafumu 8:50 nkhani