53 Popeza Inu munawapatula pa anthu onse a pa dziko lapansi akhale colowa canu, monga munanena ndi dzanja la Mose mtumiki wanu, pamene munaturutsa makolo athu m'Aigupto, Yehova Mulungu Inu.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8
Onani 1 Mafumu 8:53 nkhani