56 Wolemekezeka ndi Yehova amene anapumulitsa anthu ace Aisrayeli, monga mwa zonse analonjezazo; sanatayika mau amodzi a mau ace onse abwino, amene analankhula ndi dzanja la Mose mtumiki wace.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8
Onani 1 Mafumu 8:56 nkhani