1 Mafumu 8:61 BL92

61 Mitima yanu ikhale yangwiro ndi Yehova Mulungu wathu, kuyenda m'malemba ace ndi kusunga malamulo ace, monga lero lino.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8

Onani 1 Mafumu 8:61 nkhani