10 Ndipo kunali, zitatha zaka makumi awiri m'mene Solomo adatsiriza nyumba ziwirizo, ndizo nyumba ya Yehova ndi nyumba ya mfumu;
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 9
Onani 1 Mafumu 9:10 nkhani