1 Mafumu 9:13 BL92

13 Nati, Midzi yino mwandipatsayi njotani, mbale wanga? Naicha dzina lao, Dziko lacikole, kufikira lero lino.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 9

Onani 1 Mafumu 9:13 nkhani