1 Mafumu 9:3 BL92

3 Ndipo Yehova anati kwa iye, Ndamva pemphero lako ndi pembedzero lako wandipembedza nalo; ndapatula nyumba imene waimangayi kuikamo dzina langa nthawi zosatha, ndipo maso anga ndi mtima wanga zidzakhala kumeneko masiku onse.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 9

Onani 1 Mafumu 9:3 nkhani