43 Pamene ndinanena ndi inu simunamvera; koma munatsutsana nao mau a Yehova ndi kucita modzikuza, nimunakwera kumka kumapiri.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 1
Onani Deuteronomo 1:43 nkhani