44 Ndipo Aamori, akukhala m'mapiri muja, anaturuka kukomana ndi inu, nakupitikitsani, monga zimacita njuci, nakukanthani m'Seiri, kufikira ku Horima.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 1
Onani Deuteronomo 1:44 nkhani