Deuteronomo 1:8 BL92

8 Taonani, ndakupatsani dzikoli pamaso panu, lowani landirani dziko limene Yehova analumbirira makolo anu, Abrahamu, Isake, ndi Yakobo, kuti ili ndidzawapatsa iwo ndi mbeu zao pambuyo pao.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 1

Onani Deuteronomo 1:8 nkhani