Deuteronomo 13:14 BL92

14 pamenepo muzifunsira, ndi kulondola, ndi kufunsitsa; ndipo taonani, cikakhala coona, catsimikizika cinthuci, kuti conyansa cotere cacitika pakati pa inu;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 13

Onani Deuteronomo 13:14 nkhani