Deuteronomo 13:15 BL92

15 muzikanthatu okhala m'mudzi muja ndi lupanga lakuthwa; ndi kuuononga konse, ndi zonse ziri m'mwemo, ng'ombe zace zomwe, ndi lupanga lakuthwa.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 13

Onani Deuteronomo 13:15 nkhani