Deuteronomo 13:17 BL92

17 Ndipo pasamamatire padzanja panu kanthu ka cinthu coti cionongeke; kuti Yehova a aleke mkwiyo wacewaukali, nakucitireni cifundo, ndi kukumverani nsoni, ndi kukucurukitsani monga analumbirira makolo anu;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 13

Onani Deuteronomo 13:17 nkhani