11 Monga momwe anena malamulo akulangizani, ndi monga mwa ciweruzo akufotokozerani, mucite; mau akufotokozerani musawapatukire kulamanja kapena kulamanzere.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 17
Onani Deuteronomo 17:11 nkhani