Deuteronomo 17:12 BL92

12 Koma munthu wakucita modzikuza, osamvera wansembe wokhala ciriri kutumikirako pamaso pa Yehova Mulungu wanu, kapena woweruza, munthuyo afe; ndipo mucotse coipaco kwa Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 17

Onani Deuteronomo 17:12 nkhani