5 pamenepo muturutse mwamunayo kapena mkaziyo, anacita coipaco, kumka naye ku zipata zanu, ndiye wamwamuna kapena wamkazi; ndipo muwaponye miyala, kuti afe.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 17
Onani Deuteronomo 17:5 nkhani