16 monga mwa zonse munafunsa Yehova Mulungu wanu m'Horebe, tsiku lakusonkhana lija, ndi kuti, Tisamvenso mau a Yehova Mulungu wathu, ndipo tisaonenso mota waukuru uwu, kuti tingafe.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 18
Onani Deuteronomo 18:16 nkhani