Deuteronomo 18:6 BL92

6 Ndipo Mlevi akacokera ku mudzi wanu wina m'Israyeli monse, kumene akhalako, nakadza ndi cifuniro conse ca moyo wace ku malo amene Yehova adzasankha;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 18

Onani Deuteronomo 18:6 nkhani