Deuteronomo 18:7 BL92

7 pamenepo azitumikira m'dzina la Yehova Mulungu wace, monga amacita abale ace onse Alevi akuimirirako pamaso pa Yehova.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 18

Onani Deuteronomo 18:7 nkhani