1 Pamenepo tinabwerera, ndi kuyenda kumka kucipululu, kutsata njira ya Nyanja Yofiira, monga Yehova adanena ndi ine; ndipo tinapaza phiri la Seiri masiku ambiri.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 2
Onani Deuteronomo 2:1 nkhani