5 musalimbana nao; popeza sindikupatsakoni dziko lao, pangakhale popondapo phazi lanu ai pakuti ndapatsa Bsau phiri la Seiri likhale lace lace.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 2
Onani Deuteronomo 2:5 nkhani