Deuteronomo 21:13 BL92

13 nabvule zobvala za ukapolo wace, nakhale m'nyumba mwanu, nalire atate wace, ndi mai wace mwezi wamphumphu; ndipo atatero mulowe naye ndi kukhala mwamuna wace, ndi iye akhale mkazi wanu.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 21

Onani Deuteronomo 21:13 nkhani