Deuteronomo 21:14 BL92

14 Ndipo kudzali, mukapanda kukondwera naye, mumlole apite komwe afuna; koma musamgulitsa ndalama konse, musamamuyesa cuma, popeza wamcepetsa.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 21

Onani Deuteronomo 21:14 nkhani