15 Munthu akakhala nao akazi awiri, wina wokondana naye, wina wodana naye, nakambalira ana, wokondana naye, ndi wodana naye yemwe; ndipo mwana wamwamuna woyamba akakhala wa iye uja anadana naye;
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 21
Onani Deuteronomo 21:15 nkhani