19 azimgwira atate wace ndi mai wace, ndi kuturukira naye kwa akuru a mudzi wace, ndi ku cipata ca malo ace;
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 21
Onani Deuteronomo 21:19 nkhani