Deuteronomo 21:18 BL92

18 Munthu akakhala naye mwana wamwamuna wopulukira, ndi wopikisana naye, wosamvera mau a atate wace, kapena mau a mai wace, wosawamvera angakhale anamlanga;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 21

Onani Deuteronomo 21:18 nkhani