17 Koma azibvomereza wobadwa woyamba, mwana wa wodana naye, ndi kumwirikizira gawo lace la zace zonse; popeza iye ndiye ciyambi ca mphamvu yace; zoyenera woyamba kubadwa nzace.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 21
Onani Deuteronomo 21:17 nkhani