21 Mukawindira Yehova Mulungu wanu cowinda, musamacedwa kucicita; popeza Yehova Mulungu wanu adzakufunsani za ici ndithu ndipo mukadacimwako.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 23
Onani Deuteronomo 23:21 nkhani