Deuteronomo 24:21 BL92

21 Mutachera m'munda wanu wamphesa, musakunkha pambuyo panu; zikhale za mlendo, za mwana wamasiye, ndi za mkazi wamasiye.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 24

Onani Deuteronomo 24:21 nkhani