Deuteronomo 24:20 BL92

20 Mutagwedeza mtengo wanu wa azitona musayesenso nthambi mutatha nazo; akhale a mlendo, a mwana wamasiye, ndi a mkazi wamasiye.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 24

Onani Deuteronomo 24:20 nkhani