Deuteronomo 25:6 BL92

6 Ndipo kudzali, kuti woyamba kubadwa amene adzambala, adzalowa dzina lace la mbale wace wafayo, kuti dzina lace lisafafanizidwe m'Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 25

Onani Deuteronomo 25:6 nkhani