Deuteronomo 26:12 BL92

12 Mutatha kugawa magawo khumi, zobala zanu zonse caka cacitatu, ndico caka cogawa magawo khumi, muzizipereka kwa Mlevi, kwa mlendo, kwa mwana wamasiye, ndi kwa mkazi wamasiye, kuti adye m'midzi mwanu, ndi kukhuta.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 26

Onani Deuteronomo 26:12 nkhani