17 Mwalonjezetsa Yehova lero kuti adzakhala Mulungu wanu, ndi kuti mudzayenda m'njira zace, ndi kusunga malemba ace, ndi malamulo ace, ndi maweruzo ace, ndi kumvera mau ace.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 26
Onani Deuteronomo 26:17 nkhani