16 Lero lino Yehova Mulungu wanu akulamulirani kucita malemba ndi maweruzo awa; potero muzimvera ndi kuwacita ndi mtima wanu wonse, ndi moyo wanu wonse.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 26
Onani Deuteronomo 26:16 nkhani