15 Penyani muli mokhalamo mwanu mopatulika, m'mwamba, ndipo dalitseni anthu anu Israyeli, ndi nthaka imene munatipatsa, monga munalumbirira makolo athu, dziko moyenda mkaka ndi uci ngati madzi.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 26
Onani Deuteronomo 26:15 nkhani