14 Sindinadyako m'cisoni canga, kapena kucotsako podetsedwa, kapena kuperekako kwa akufa; ndamvera mau a Yehova Mulungu wanga; ndacita monga mwa zonse munandilamulira ine.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 26
Onani Deuteronomo 26:14 nkhani