7 Pamenepo tinapfuulira kwa Yehova, Mulungu wa makolo athu; ndipo Yehova anamva mau athu, napenya kuzunzika kwathu, ndi nchito yathu yolemetsa, ndi kupsinjika kwathu;
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 26
Onani Deuteronomo 26:7 nkhani