10 Potero muzimvera mau a Yehova Mulungu wanu, ndi kucita malamulo ace, ndi malemba ace, amene ndikuuzani lero lino.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 27
Onani Deuteronomo 27:10 nkhani