9 Ndipo Mose, ndi ansembe Alevi ananena ndi Israyeli wonse, ndi kuti, Khalani cete, imvanitu, Israyeli; lero lino mwasanduka mtundu wa anthu wa Yehova Mulungu wanu.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 27
Onani Deuteronomo 27:9 nkhani