10 Muimirira inu nonse lero lino pamaso pa Yehova Mulungu wanu; mafumu anu, mapfuko anu, akuru anu, ndi akapitao anu, amuna onse a Israyeli;
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 29
Onani Deuteronomo 29:10 nkhani