Deuteronomo 29:20 BL92

20 Yehova sadzamkhululukira, koma pamenepo mkwiyo wa Yehova ndi nsanje yace zidzamfukira munthuyo; ndipo temberero lonse lolembedwa m'buku ili lidzamkhalira; ndipo Yehova adzafafaniza dzina lace pansi pa thambo.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 29

Onani Deuteronomo 29:20 nkhani