21 Ndipo Yehova adzamsiyanitsa ndi mafuko onse a Israyeli ndi kumcitira coipa, monga mwa matemberero onse a cipangano colembedwa m'buku ili la cilamulo.
Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 29
Onani Deuteronomo 29:21 nkhani