Deuteronomo 29:22 BL92

22 Ndipo mbadwo ukudza, ana anu akuuka mutafa inu, ndi mlendo wocokera ku dziko lakutali, adzati, pakuona iwo miliri ya dziko ili, ndi nthendazi; Yehova awadwalitsa nazo,

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 29

Onani Deuteronomo 29:22 nkhani