Deuteronomo 29:23 BL92

23 ndi kuti lidapsa dziko lace lonse ndi sulfure, ndi mcere, kuti sabzalamo, kapena siliphukitsa kanthu kapena sumerapo msipu, monga kupasula kwace kwa Sodomu ndi Gomora, Adima, ndi Zeboimu, imene Yehova anaipasula m'mkwiyo wace ndi ukali wace;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 29

Onani Deuteronomo 29:23 nkhani